Taitanic movie

Taitanic movie Titanic movie it's a true story

19/04/2023

TITANIC SHIP
*The ship of today and tomorrow*

Titanic ndi sitima yaikulu yapamadzi yomwe idamira pa 15 April mu 1912 lolemba (Monday) kum'bandakucha. Kumpoto kwanyanja ya Atlantic.

"Ngakhale mulungu sangamize sitimayi" adatero Mr. Bruce Ismay atafunsidwa zakulimba mtima kwake popanga sitima ya Titanic mu 1908.
It's Ishmael Losani kujama live za titanic ๐Ÿšข ๐Ÿšข ๐Ÿšข ๐Ÿšข ๐Ÿšข unsunk.

Mu 1909 kampani yotchedwa White Star Line idayamba ntchito yopanga masitima atatu akuluakulu kwambiri;
1). Jigate Ship
2). Olympic Ship
3). Titanic Ship

Mu chakacho 1909, akatswiri odziwa kupanga sitima zapamadzi a *Harland & Wolf* ku Belfast, adaiyamba ntchito yokonza sitima za Olympic ndi Titanic.

Pakutha pazaka zitatu ntchito yokonza sitimazi idamalizika, ndipo lidafika tsiku loti sitimazo ziende ulendo wa wautali. Lidali kachitatu (Wednesday) pa 10 April 1912, pomwe padakonzedwa kuti sitimazi ziende ulendo wautali uja. Pomwe sitima ya Titanic inkalowera ku New York city ku America ๐Ÿ‡ป๐Ÿ‡ฎ kuchoka ku Southampton ku England ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ง.

*ZIDAKHALA MOTANI ZA TITANIC?*

Mu sitimayi mudali zinthu zosangalatsa kwambiri monga Makanema, Gym, Ma barber shop, ma shower ๐Ÿšฟ, malo ogulira zinthu mowa ndi zakumwa zoziziritsa kukhosi zidali momwemo, mudali mwamsika ndithu komanso mudali zipinda zogonamo (Rest houses).

Oyendetsa sitimayi Captain Edward J Smith adailiza, ndipo sitimayi idanyamuka pa Belfast Iceland ku Southampton mdziko La ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ง Britain ulendo uja waku New York mdziko LA ๐Ÿ‡ป๐Ÿ‡ฎ America.

Sitimayi idanyamuka lachitatu pa 10 April 1912. Ulendo ulimkati musitimayi mudabuka moto omwe aliense sadauone ndipo palibe amene adazindikira kuti sitimayo ikuyaka, pamepo nkuti pali pa 12 April lachisanu mu 1912.

Motowo unkayaka pang'onooang'ono pansi penipeni chakumanja, nkumakolera ndithu wakumbuyo kumanja komweko. Panthawiyo nkuti musitimayi muli zisangalalo zamnanuุŒ kudyerera kumwerera kuvina mmenemo.

Kufikira pa lamulungu pa 14 April 1912, motowo unkangoyakabe, ndipo palibe adatulukirabe zamotowo. Apa nkuti anthu musitimamo adali pachisangalalo chosasimbika pomwe Captain Edward J Smith adaipatsa moto, nde inkathamanga Titanic liwiro losaerekezera. Mwadzidzidzi Captain adaona chimwala chamadzi ouma (Iceberg).

Mwaukadaulo Captain Edo adayesa kuti azembe mwalawo koma liwiro la Sitima komanso adali atayandikira Kale, mmalo mwake Edo adangoti chichitike uku akuserabe kulambalala mwalawo.

Pali nkhani apa....... Next!



Osaiwala kupanga Like page ya Ishmael Losani

Address

London

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Taitanic movie posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category